Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Numeri 26:62 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo owerengedwa ao ndiwo zikwi makumi awiri mphambu zitatu, mwamuna yense wa mwezi umodzi ndi mphambu; popeza sanawerengedwa pakati pa ana a Israyeli; cifukwa sanawapatsa colowa mwa ana a Israyeli.

Werengani mutu wathunthu Numeri 26

Onani Numeri 26:62 nkhani