Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Numeri 26:59 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo dzina lace la mkazi wace wa Amiramu ndiye Yokebedi, mwana wamkazi wa Levi, wobadwira Levi m'Aigupto; ndipo iye anambalira Amiramu Aroni ndi Mose, ndi Miriamu mlongo wao.

Werengani mutu wathunthu Numeri 26

Onani Numeri 26:59 nkhani