Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Numeri 26:35 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ana amuna a Efraimu monga mwa mabanja ao ndiwo: Sutela, ndiye kholo la banja la Asutela; Bekeri, ndiye kholo la banja la Abekeri; Tahana, ndiye kholo la banja la Atahana.

Werengani mutu wathunthu Numeri 26

Onani Numeri 26:35 nkhani