Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Numeri 26:20 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo ana a Yuda monga mwa mabanja ao ndiwo: Sela, ndiye kholo la banja la Asela; Perezi, ndiye kholo la banja la Aperezi; Zera, ndiye kholo la banja la Azera.

Werengani mutu wathunthu Numeri 26

Onani Numeri 26:20 nkhani