Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Numeri 26:15 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ana amuna a Gadi monga mwa mabanja ao ndiwo: Zefoni, ndiye kholo la banja la Azefoni; Hagi, ndiye kholo la banja la Ahagi; Suni, ndiye kholo la banja la Asuni;

Werengani mutu wathunthu Numeri 26

Onani Numeri 26:15 nkhani