Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Numeri 25:6 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo, taonani, anadza wina wa ana a Israyeli, nabwera naye mkazi Mmidyani kudza naye kwa abale ace, pamaso pa Mose, ndi pamaso pa khamu lonse la ana a Israyeli, pakulira iwo pa khomo la cihema cokomanako.

Werengani mutu wathunthu Numeri 25

Onani Numeri 25:6 nkhani