Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Numeri 25:18 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

popeza akusautsani ndi manyengo ao amene anakunyengani nao; m'cija ca Peori, ndi ca Kozibi, mwana wamkazi wa kalonga wa ku Midyani, mlongo wao, amene adamupha tsiku la mliri, m'cija ca Peori.

Werengani mutu wathunthu Numeri 25

Onani Numeri 25:18 nkhani