Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Numeri 24:23-25 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

23. Ndipo ananena fanizo lace, nati,Ha! adzakhala ndi moyo ndani pakucita ici Mulungu?

24. Koma zombo zidzafika kucokera ku doko la Kitimu,Ndipo adzasautsa Asuri, nadzasautsa Ebere,Koma iyenso adzaonongeka.

25. Ndipo Balamu anauka, namuka nabwerera kumalo kwace; ndi Balaki yemwe anamka njira yace.

Werengani mutu wathunthu Numeri 24