Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Numeri 23:4 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pamenepo Mulungu anakomana ndi Balamu; ndipo ananena ndi iye, Ndakonza maguwa a nsembe asanu ndi awiri, ndipo ndapereka ng'ombe ndi nkhosa yamphongo pa guwa la nsembe liri lonse.

Werengani mutu wathunthu Numeri 23

Onani Numeri 23:4 nkhani