Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Numeri 23:13 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Balaki anati naye, Tiyetu, upite nane kumalo kwina, kumene ukawaona; udzaona malekezero ao okha, osawaona onse; ndipo pokhala pamenepo ukanditembererere iwo.

Werengani mutu wathunthu Numeri 23

Onani Numeri 23:13 nkhani