Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Numeri 22:8 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo ananena nao, Mugone kuno usiku uno, ndidzakubwezerani mau, monga Yehova adzanena ndi ine; pamenepo mafumu a Moabu anagona ndi Balamu.

Werengani mutu wathunthu Numeri 22

Onani Numeri 22:8 nkhani