Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Numeri 22:34 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pamenepo Balamu anati kwa mthenga wa Yehova, Ndacimwa, popeza sindinadziwa kuti munaima mondiletsa m'njira; ndipo tsopano, ngati cikuipirani, ndibwerera.

Werengani mutu wathunthu Numeri 22

Onani Numeri 22:34 nkhani