Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Numeri 21:9 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Mose anapanga njoka yamkuwa, naiika pamtengo; ndipo kunali, njoka itamluma munthu ali yense, nakapenyetsetsa iye pa njoka yamkuwa, nakhala ndi moyo.

Werengani mutu wathunthu Numeri 21

Onani Numeri 21:9 nkhani