Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Numeri 21:23 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Sihoni sanalola Israyeli apitire m'malire ace; koma Sihoni anamemeza anthu ace onse, nadzakomana naye Israyeli m'cipululu, nafika ku Jahazi, nathira nkhondo pa Israyeli.

Werengani mutu wathunthu Numeri 21

Onani Numeri 21:23 nkhani