Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Numeri 20:28 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Mose anabvula Aroni zobvala zace, nabveka Eleazara mwana wace; ndipo Aroni anafa pomwepo pamwamba pa phiri, Pamenepo Mose ndi Eleazara anatsika m'phirimo.

Werengani mutu wathunthu Numeri 20

Onani Numeri 20:28 nkhani