Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Numeri 20:24 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Aroni adzaitanidwa kumka kwa anthu a mtundu wace; pakuti sadzalowa m'dziko limene ndapatsa ana a Israyeli, popeza munapikisana ndi mau anga ku madzi a Meriba.

Werengani mutu wathunthu Numeri 20

Onani Numeri 20:24 nkhani