Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Numeri 20:19 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo ana a Israyeli ananena naye, Tidzatsata mseu; ndipo tikakamwa madzi ako, ine ndi zoweta zanga, pamenepo ndidzapatsa mtengo wace; sindifuna kanthu kena koma kungopitapo mwa njira.

Werengani mutu wathunthu Numeri 20

Onani Numeri 20:19 nkhani