Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Numeri 20:10 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Mose ndi Aroni anasonkhanitsa msonkhano pathanthwe, nanena nao iye, Tamvanitu, opikisana naye inu; kodi tikuturutsireni madzi m'thanthwe umu?

Werengani mutu wathunthu Numeri 20

Onani Numeri 20:10 nkhani