Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Numeri 19:13 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ali yense wakukhudza mtembo wa munthu ali yense wakufa, osadziyeretsa, aipsa kacisi wa Yehova; amsadze munthuyo kwa Israyeli; popeza sanamwaza madzi akusiyanitsa; ndiye wodetsedwa; kudetsedwa kwace kukali pa iye.

Werengani mutu wathunthu Numeri 19

Onani Numeri 19:13 nkhani