Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Numeri 19:10 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo wakuola mapulusayo a ng'ombe ya msoti atsuke zobvala zace, nadzakhala wodetsedwa kufikira madzulo; ndipo likhale lemba losatha kwa ana a Israyeli, ndi kwa mlendo wakukhala pakati pao.

Werengani mutu wathunthu Numeri 19

Onani Numeri 19:10 nkhani