Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Numeri 18:9 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Izi ndi zako pa zinthu zopatulikitsa, zosafika kumoto; zopereka: zao zonse, ndi nsembe zao zonse zaufa, ndi nsembe zao zonse zaucimo, ndi nsembe zao zonse zoparamula, zimene Andibwezera Ine, zikhale zopatulikitsa za iwe ndi za ana ako amuna.

Werengani mutu wathunthu Numeri 18

Onani Numeri 18:9 nkhani