Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Numeri 18:28 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Momweno inunso muzipereka kwa Yehova nsembe yokweza yocokera ku magawo anu onse a magawo khumi, a zonse muzilandira kwa ana a Israyeli; ndipo muperekeko nsembe yokweza ya Yehova kwa Aroni wansembe.

Werengani mutu wathunthu Numeri 18

Onani Numeri 18:28 nkhani