Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Numeri 18:24 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Popeza ndapatsa Alevi limodzi la magawo khumi, la ana a Israyeli, limene apereka nsembe, yokweza kwa Yehova, likhale colowa cao; cifukwa cace ndanena nao, Asadzakhale naco colowa mwa ana a Israyeli.

Werengani mutu wathunthu Numeri 18

Onani Numeri 18:24 nkhani