Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Numeri 18:21 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo taonani, ndawaninkha ana a Levi limodzi la magawo khumi mwa zonse m'Israyeli, likhale colowa cao, mphotho ya pa nchito yao alikuicita, nchito ya cihema cokomanako.

Werengani mutu wathunthu Numeri 18

Onani Numeri 18:21 nkhani