Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Numeri 18:19 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Nsembe zokweza zonse za zinthu zopatulika, zimene ana a Israyeli azikweza kwa Yehova, ndazipereka kwa iwe, ndi kwa ana ako amuna ndi kwa ana ako akazi pamodzi ndi iwe, likhale lemba losatha; ndilo pangano lamcere losatha, pamaso pa Yehova, kwa iwe ndi mbeu zako pamodzi ndi iwe.

Werengani mutu wathunthu Numeri 18

Onani Numeri 18:19 nkhani