Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Numeri 18:16 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo zimene ziti zidzaomboledwa uziombole kuyambira za rowezi umodzi, monga mwa kuyesa kwako, pa ndarama za masekeli asanu, kuyesa sekeli wa malo opatulika, ndiwo magera makumi awiri.

Werengani mutu wathunthu Numeri 18

Onani Numeri 18:16 nkhani