Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Numeri 18:1 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Yehova anati kwa Aroni, Iwe ndi ana ako amuna ndi banja la kholo lako pamodzi ndi iwe muzisenza mphulupulu ya malo opatulika; ndipo iwe ndi ana ako amuna pamodzi ndi iwe musenze mphulupulu ya nchito yanu ya nsembe.

Werengani mutu wathunthu Numeri 18

Onani Numeri 18:1 nkhani