Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Numeri 17:8 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo kunali m'mawa mwace, kuti Mose analowa m'cihema ca mboni; ndipo taonani, ndodo ya Aroni, ya pa banja la Levi, inaphuka, nionetsa timaani, nicita maluwa, nipatsa akatungurume.

Werengani mutu wathunthu Numeri 17

Onani Numeri 17:8 nkhani