Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Numeri 17:6 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Mose ananena ndi ana a Israyeli, ndipo akalonga ao onse anapereka, yense ndodo imodzi, monga mwa mabanja a makolo ao, ndodo khumi ndi ziwiri; ndi ndodo ya Aroni inakhala pakati pa ndodo zao.

Werengani mutu wathunthu Numeri 17

Onani Numeri 17:6 nkhani