Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Numeri 16:9 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

kodi muciyesa cinthu cacing'ono, kuti Mulungu wa Israyeli anakusiyanitsani ku khamu la Israyeli, kukusendezani pafupi pa iye, kucita nchito ya kacisi wa Yehova, ndi kuima pamaso pa khamu kuwatumikira;

Werengani mutu wathunthu Numeri 16

Onani Numeri 16:9 nkhani