Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Numeri 16:48-50 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

48. Ndipo anaima pakati pa akufa ndi amoyo; ndi mliri unaleka.

49. Koma akufa nao mliri ndiwo zikwi khumi ndi zinai mphambu mazana asanu ndi awiri, osawerenga aja adafera cija ca Kora.

50. Ndipo Aroni anabwera kwa Mose ku khomo la cihema cokomanako; ndi mliri unaleka.

Werengani mutu wathunthu Numeri 16