Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Numeri 16:46 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Mose anati kwa Aroni, Tenga mbale yako yofukiza, nuikemo mota wa ku guwa la nsembe, nuikepo cofukiza, nufulumire kumuka ku khamulo, nuwacitire cowatetezera; pakuti waturuka mkwiyo pamaso pa Yehova; wayamba mliri.

Werengani mutu wathunthu Numeri 16

Onani Numeri 16:46 nkhani