Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Numeri 16:22 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo anagwa nkhope zao pansi, nati, Mulungu, ndinu Mulungu wa mizimu ya anthu onse, walakwa munthu mmodzi, ndipo kodi mukwiya nalo khamu lonse?

Werengani mutu wathunthu Numeri 16

Onani Numeri 16:22 nkhani