Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Numeri 16:17 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

nimutenge munthu yense mbale yace yofukizamo, nimuike cofukiza m'mwemo, nimubwere nazo, yense mbale yace yofukizamo pamaso pa Yehova, mbale zofukizamo mazana awiri ndi makumi asanu; ndi iwe, ndi Aroni, yense mbale yace yofukizamo.

Werengani mutu wathunthu Numeri 16

Onani Numeri 16:17 nkhani