Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Numeri 14:29 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

mitembo yanu idzagwa m'cipululu muno; ndi owerengedwa anu onse, monga mwa kuwerenga kwanu konse, kuyambira a zaka makumi awiri ndi mphambu, akudandaula pa Ine;

Werengani mutu wathunthu Numeri 14

Onani Numeri 14:29 nkhani