Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Numeri 14:18 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Yehova ndiye wolekereza, ndi wa cifundo cocuruka, wokhululukira mphulupulu ndi kulakwa, koma wosamasula woparamula; wakuwalanga ana cifukwa ca mphulupulu ya atate ao, kufikira mbadwo wacitatu ndi wacinai.

Werengani mutu wathunthu Numeri 14

Onani Numeri 14:18 nkhani