Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Numeri 14:14 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

ndipo adzawauza okhala m'dziko muno; adamva kuti inu Yehova muli pakati pa anthu awa; pakuti muoneka mopenyana, Yehova, ndi mtambo wanu umaima pamwamba pao, ndipo muwatsogolera, ndi mtambo njo msana, ndi moto njo usiku.

Werengani mutu wathunthu Numeri 14

Onani Numeri 14:14 nkhani