Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Numeri 13:26 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo anamuka, nadza kwa Mose, ndi Aroni, ndi khamu lonse la ana a Israyeli, ku cipululu ca Parana ku Kadesi; ndipo anabwezera mau iwowa, ndi khamu lonse, nawaonetsa zipatso za dzikoli.

Werengani mutu wathunthu Numeri 13

Onani Numeri 13:26 nkhani