Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Numeri 13:13-16 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

13. Wa pfuko la Aseri, Setri mwana wa Mikayeli.

14. Wa pfuko la Nafitali, Nabi mwana wa Vopisi.

15. Wa pfuko la Gadi, Geyuelimwana wa Maki.

16. Awandi maina a amunawo Mose anawatumira azonde dziko. Ndipo Mose anamucha Hoseya mwana wa Nuni Yoswa.

Werengani mutu wathunthu Numeri 13