Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Numeri 12:14 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Yehova anati kwa Mose, Atate wace akadamlabvulira malobvu pankhope pace sakadacita manyazi masiku asanu ndi awiri? ambindikiritse kunja kwa cigono masiku asanu ndi awiri; ndipo atatero amlandirenso.

Werengani mutu wathunthu Numeri 12

Onani Numeri 12:14 nkhani