Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Numeri 12:10 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo mtambo unacoka pacihema; ndipo taonani, Miriamu anali wakhate, wa mbu ngati cipale cofewa; ndipo Aroni anapenya Miriamu, taonani, anali wakhate.

Werengani mutu wathunthu Numeri 12

Onani Numeri 12:10 nkhani