Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Numeri 11:31 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo kudacokera mphepo kwa Yehova, nidza nazo zinziri zocokera kunyanja, nizitula kucigono, ulendo wa tsiku limodzi dera lino, ndi ulendo wa tsiku limodzi dera lina, pozungulira pa cigono, ndipo zinabisa nthaka ngati muyeso wa mikono iwiri.

Werengani mutu wathunthu Numeri 11

Onani Numeri 11:31 nkhani