Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Numeri 11:25 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Yehova anatsika mumtambo, nanena nave, natengako mzimu uli pa iye, nauika pa akuru makumi asanu ndi awiri; ndipo kunali kuti pokhala mzimu pa iwowa, ananenera; koma osabwerezanso.

Werengani mutu wathunthu Numeri 11

Onani Numeri 11:25 nkhani