Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Numeri 11:1 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo anthu anaipa, namadandaula m'makutu a Yehova; ndipo pamene Yehova anamva anapsa mtima; ndi mota wa Yehova unayaka pakati pao, nunyeketsa ku cilekezero ca cigono.

Werengani mutu wathunthu Numeri 11

Onani Numeri 11:1 nkhani