Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Numeri 10:33 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo anayenda kucokera ku phiri la Yehova ulendo wa masiku atatu; ndipo likasa la cipangano ca Yehova, linawatsogolera ulendo wa masiku atatu kuwafunira popumulira.

Werengani mutu wathunthu Numeri 10

Onani Numeri 10:33 nkhani