Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Numeri 10:3-5 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

3. Akaliza, khamu lonse lisonkhane kuli iwe ku khomo la cihema cokomanako,

4. Akaliza limodzi, pamenepo akalonga, akuru a zikwi a m'Israyeli, azisonkhana kuli iwe.

5. Mukaliza cokweza, ayende a m'zigono za kum'mawa.

Werengani mutu wathunthu Numeri 10