Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Numeri 10:29 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Mose anati kwa Hobabu mwana wa Reueli Mmidyani mpongozi wa Mose, Ife tirikuyenda kumka ku malo amene Yehova anati, Ndidzakupatsani awa; umuke nafe, tidzakucitira zokoma; popeza Yehova wanenera Israyeli zokoma.

Werengani mutu wathunthu Numeri 10

Onani Numeri 10:29 nkhani