Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Numeri 10:1-3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

1. Ndipo Yehova ananena ndi Mose, nati,

2. Dzipangire malipenga awiri asiliva; uwasule mapangidwe ace; ucite nao poitana khamu, ndi poyendetsa a m'zigono.

3. Akaliza, khamu lonse lisonkhane kuli iwe ku khomo la cihema cokomanako,

Werengani mutu wathunthu Numeri 10