Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Numeri 1:46-48 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

46. inde owerengedwa onse ndiwo zikwi mazana asanu ndi limodzi mphambu zitatu kudza mazana asanu ndi makumi asanu.

47. Koma Alevi monga mwa pfuko la makolo ao sanawerengedwa mwa iwo.

48. Popeza Yehova adalankhula ndi Mose, ndi kuti,

Werengani mutu wathunthu Numeri 1