Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Nehemiya 9:36 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Tapenyani, ife lero ndife akapolo, ndi dzikoli mudalipereka kwa makolo athu kudya zipatso zace ndi zokoma zace, taonani, ife ndife akapolo m'menemo.

Werengani mutu wathunthu Nehemiya 9

Onani Nehemiya 9:36 nkhani